Mfumukazi
Be Welcomed, Be Pampered, Be YOU!
~Mfumukazi
21/07/2026
Sale sale sale
We are in LL, kutali timatumiza
0888172027
K35,000 each
Available in LL Area 18A.
Kutali timatumiza.
13/06/2026
Skirt K55,000
Area 18A
0888172027
Visit our shop in Area 18A.
We are next to the Tower
Call or Whatsapp 0888172027
01/07/2025
Dudu Osun black soap is available now both in Limbe and Lilongwe. Soap othana ndi mavuto onse apakhungu. Aliyense atha kusambira ana komanso akulu.
K15,000 each
0888172027
30/06/2025
Amen
27/06/2025
Nsalu za Congo, 6 yards available in Lilongwe K45,000 cash, kutali timatumiza.
Zipezeka ku shop yathu ku Limbe on Monday 30th June 2025.
Whatsapp 0888172027
19/06/2025
Dear Customers,
We’re excited to let you know that Mfumukazi Shop is now open in Area 18A, Lilongwe!
Wokondeka ma customer athu,
Tafuna kukudziwitsani kuti tatsegula shop mu Lilongwe, ku Area 18A
Tili pafupi ndi ma shop ama Bulundi, pa chi tower.
From the Area 10 traffic lights, go down the cemetary road. Mukafika pa hump yachiwiri, take the left turn pomwepo mupeza shop yathu.
ma nambala athu nawa
0888 17 20 27
We look forward to seeing you!
Wokondeka ma customer athu,
Tafuna kukudziwitsani kuti tatsegula salon mu Lilongwe, ku Area 18A pafupi ndi ma shop ama Bulundi, pa chi tower.
From the Area 10 traffic lights, go down the cemetary road. Mukafika pa hump yachiwiri, take the left turn pomwepo mupeza shop yathu.
ma nambala athu nawa 0888 17 20 27 komanso 0999172027
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Blantyre
Opening Hours
| Monday | 08:00 - 18:00 |
| Tuesday | 08:00 - 18:00 |
| Wednesday | 08:00 - 18:00 |
| Thursday | 08:00 - 18:00 |
| Friday | 07:00 - 18:00 |
| Saturday | 09:00 - 17:00 |
