Billy's House Studios

Billy's House Studios

Share

WE SAIL WITH THE PREVAILING WINDS OF ART

•Your hub for international News, compelling Documentaries, and captivating Media Shows.

We also empower rising stars in Music and Acting through expert Video and Audio Production services

Photos from Billy's House Studios's post 24/09/2026

Mkulu wa TNM, Lloyd Gowera, wanena kuti mafoni awiri okha omwe anali a anthu omwe anali m’ndege yomwe inagwa ku Chikangawa ndi omwe anasonyeza kulumikizana komaliza kodziwika bwino ndi ma tower a TNM.
Kampaniyo yawuza Ad Hoc Committee yomwe ikufufuza za ngoziyi kuti mafoniwo anali a Daniel Kanyemba ndi Major Aidin.

Gowera wanena kuti foni ya Major Aidin inasonyeza kuti inali italumikizana komaliza ndi tower ya TNM ku Mzimba turn-off nthawi ya 11:11 m'mawa pa 10 June 2024. Pamene foni ya Kanyemba inasonyeza kulumikizana komaliza ku Nthungwa Tower nthawi ya 10:16 m'mawa.

Iye wanenanso kuti TNM sinapatsidwe manambala a mafoni a anthu omwe anali m’ndegeyo, chifukwa ambiri mwa anthuwo sanali makasitomala a TNM. M’malo mwake, pa 11 June, kampaniyo idagwiritsa ntchito zolemba za KYC (Know Your Customer) kuti izindikire manambala omwe analembedwa ndi anthu omwe mayina awo anali pa mndandanda wa anthu omwe anali m’ndegeyo.

(Wolemba: Grant C.E.O)

23/09/2026

16/09/2026

🙄

07/09/2026

MANEB iweyo 😂🙌💔

31/08/2026

Mwana Uyu Akuwonesatu. 🔥🔥

27/08/2026

Ati Mpira Wasikana Ndi Ganja💔🙌??

'shousestudios

26/08/2026

Nyimbo Ya Skhrizy Ija Sizokuti Wanyoza Temwa Ekha Ayi Koma Asikana Onse Amene Alindi Amawonekedwe Achimuna Si Temwa TC6 Chawinga Ekha Ayi🙄

24/08/2026

MALAWI vs SKHRIZY
🙌😂💔

24/08/2026

Koma Anthu 🙌😂💔
Temwa TC6 Chawinga

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Zomba?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Website

Address

Non
Zomba

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Billy's House Studios posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Subscribe

We will notify you when anything happens in Zomba.