Ungwazi
Nasanganya wazinthu
kuchimpwilikiti
kumpanipani kwenikweni
Imfa iweyo💔🙌🏾kusiya ulemero wosewu munthu kumakalowa pa dothi🙌🏾
Tiyeni tiziyenda okhonzeka shuwa
Follow Ungwazi
01/10/2026
Tawonani billionaire akuyenda mujumbo💔Moyo supanganika 🙌🏾ukakhala ndimoyo umakhala ndi choice choyankha koma ukamwalira umakhala ulibe Yes or No🙌🏾tiziyenda okonzeka🙌🏾
Follow Ungwazi
01/10/2026
Wickney Chivayo Zimbabwean richest business man dies in helicopter ndinkazi wake Lucy (Lulu)
Nde check zithuzi kuma comment 👇🏽
Moyo supanganika uyuu🙌🏾
Follow Ungwazi
Koma abale uwuwu simulandu koma? Uyuyu akanamangidwa izizi sizowona💔
Follow Ungwazi for more
10/09/2026
Sad news💔
Ku South Africa dera la George Munthu wamwalilira kuganyu anamuyitana ganyu azinzake akuti amakumba pipe then kenako analowa kuti a kiline pipe yo then nthaka inasweka nkuwakwirila wina mutu umawoneka koma agondwewa anali pansi panthaka ndiye zinavuta kuti awapulumutse ndimmene wafera mzathuyi
Mzimu wa Victor Gondwe ukause mtendere💔🕊
Kodi ukuso mukuwelenga ma weeding dress?
Congratulations Onesmus
25/08/2026
A President a ku USA Donald Trump, wati mbendela ya US isitsidwe ku US kwa one week popeleka ulemu kwa Dolly Parton, yemwe wamwalira lero ali ndi dzaka 80. Mzimu wake ukause mtendere💔
Anayimba nyimbo ya
It's too late
Coat of my colors
Silver and gold
Think of Love
Jolene
Ndinyimbo zambiri💕💕
21/08/2026
Ndiangati omwe sitimaziwa kuti alindimwana wasize yimeneyi?
Happy happy blessed birthday to Ovilera Longwe
💕💕
Follow Ungwazi
Mwana wa 8 years kucapetown wazipha ndichingwe cha pajama (chovala chogonera) chomwe waziphera sichikuziwika mwana wanzathu wakuMalawi Ambuye atonthoze makolo ake💔💔
Follow Ungwazi for more news
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Mzimba
......
Alerts
Be the first to know and let us send you an email when Ungwazi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.
