Somo Bridal Store

Somo Bridal Store

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Somo Bridal Store, Beauty Store, Machinjiri Nthawila, Blantyre.

25/08/2026

komano ndili ndi funso,,,,mutha kukwatirana ndi mamuna or mkazi Oti iyeyo amakukondani koma azibale Ake sakufunani mkomwe?

Photos from Somo Bridal Store's post 24/08/2026

Happy Anniversary kwa bride wathu,. Inu chonchi ayi?πŸ€£πŸ™πŸ™Œ.

Contact us on 0988449160
Somo Bridal Store

Photos from Somo Bridal Store's post 24/08/2026

ukwati usakanike chifukwa dress yokupangani fit sikupezeka tipezeni ife a Somo Bridal Store tili Ndima plus size Abwino abwino

we're located in Blantyre Machinjiri Nthawila

whatsApp/ call +265988449160

24/08/2026

Somo Bridal Store is here to for you. We deliver our services paliponse muno Malawi.

23/08/2026

Tiyankhuleni ife a Somo Bridal Store kuti tizawalitse ukwati wanu ndi ma wedding dresses apamwamba.

23/08/2026

Mwadzuka bwanji Akasi?,, Zonsezi zikutheka ndi ife a Somo Bridal Store.

22/08/2026

Lero tikupanga za bride wathu. Tiyankhuleni ife a Somo Bridal Store tiyendetse nkhani yakavalidwe ka Mkwatibwi wanu.

Photos from Somo Bridal Store's post 22/08/2026

6:00 AM, Kuno ku Somo Bridal Store kwacha bwino Kaya anzathu kumeneko?. mpatseni ka like basi.


Somo Bridal Store

Photos from Somo Bridal Store's post 21/08/2026

Bride wathu feeling comfortable, Pajatu tinati ma morning gowns tili nawonso πŸ˜‚..Or mutakhala inu kukwiyako uyambira pati.πŸ₯°πŸ˜˜

Somo Bridal Store
0988449160

21/08/2026

lero mubwera?

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Machinjiri Nthawila
Blantyre