TRY Skills Experience

TRY Skills Experience

Share

Empowering beauty, one style at a time.

TRYSKILLS EXPERIENCE offers top-notch cosmetology training to help you unleash your creativity and turn your passion into a career. 💇

10/04/2026
08/04/2026

khani yabwino kwanonse.Tangoganizani muli ndisalon yanu yabwino kapena mukugwila ntchito pa salon ya Executive mukukupha mwakwacha ochuluka.Mwini wasalon sakhala osadziwa zatsitsi mudula anthu matsitsi zaphuzileni knowledge. Salon sitilemba munthu oti sanapangoko zasalon

Tabwelani mudzaphuzile kumanga tsitsi zosiyanasiyapa,pedicure & manicure(kuchotsa zikang'a) makeup(kuphoda)kutsuka mutu mwandondomeko,retouch yoyenelera,kupanga mawig,kachotsedwe kafundu,kuika marollez,kutinta tsitsi,kapakidwe kamafuta koyenelera,zaphuzileni zamatsitsi osiyasiya ndizana zambiri zamusalon.

Tangoganizanizani zosezitu pamtengo wa zii ndipo umalipila pang'onopang'o.Kumaliza schooltu sikumangokhala pakhomo kukhala mzimai ongokhala lero ai.Ubwino wake timaphuzitsa aliyese ndiothela school kuprimary umatha kukhala udzidalira pawekha.Fees K200000 registration K10 000 Till Ku Lilongwe bwelani

06/04/2026

Amayi ndiachinyamata tavetselani bwino.Yambani ulendo wanu ndi TRY SKILLS EXPERIENCE. Kumene kuli maphuziro abwino opindulitsa moyo wanu
Kutsegula salon sikulira zambiri ndipo umapha makwacha ochuluka ngati ukudziwa chochita. Dzaphuzileni Theory and practical kumanga Brazilian knots braids,Twist,smart different lines, Pedicure and manicure, kusoka mawig ndikumanga zosiyanasiya. Dzaphuzileni wash &set, Retouch,Facial, massage therapy, hair color and hair highlights,Gel Nails, Makeup ndizina zambiri zokhudzana ndisalon.

Mwiniwaketu wasalon sakhala osadziwa kalikose, umangopeza macustomer onse akuthawa chifukwa cholembaso anthu atchito ogodziwa kumanga koma zachemicals sanaphuzileko mpang'ono pomwe.
Dzaphuzileni nose lero.Ubwino waschool yathu ndiyawina aliyese yemwe Ali ndichidwi chophuzila ma skills okhudzana ndizasalon.

Timaphuzitsaso mmene mungayambile business ya salon,Mmene mungafunile ntchito,kapezedwe macustomer,kuyamba mobile salon,Customer care,kamangidwe kaana ndizina zambiri.

Fees yathu ndisaboola thumba ndiyotsika kwambiri.Umapeleka pang'onopang'ono kwinaku ukuphuzila.Dzalembetseni lero near st Johns Catholic secondary school. Registration fee K10 000. #+265 984474117/0891524291

06/04/2026

Get professional Training, Get paid.
Learn from the Best,Become the Best
Where Art meet Beauty
Beauty school for lifetime
Transform looks,Transforming Beauty
Get salon -Ready with TRY SKILLS EXPERIENCE
Transform your passion with career Registration K10 000

17/12/2024

Therapeutic Pedicure🌺

17/12/2024

Tryskills students

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


Area 36 Street Johns Catholic Church, Opposite Chroma Next Prince Mo P. V. T School
Lilongwe

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 17:00