ABU shabaabu

ABU  shabaabu

Share

Ansalam alaikum warahmatullah wabarakaatuh

18/10/2024
18/10/2024

Ndiye mwati kuzinga ng'ombe yomwe inali yabere after kuzinga ndikupeza kamwana mmimbamo katafa

Sharia ikuti chani zakamwanako?🙄

29/07/2023

اللهم لك الحمد والشكر

20/11/2022

Umoyo wandiphuzisa kuti
Munthu ukafuna kulila kamba kamavuto uzingolowa nyumba ndikukhala pakona yanyumbayo ndikumalila ukamaliza kulila utuluke panja utazipukutapukuta misozi bas
Kugulu laanthu utuluke ukumwetulila

Plz olo mavuto akule bwanji musapange chiganizo chochosa moyo wanu osazipha plz kuzipha ndi nsambi

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Ndirande?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


Nchalo
Ndirande