MANZY SA
NTHABWALA
Eee koma ku mudzi anakoza amagulitsa Nkhuku kuti agule ndiwo
πππππππππππ
Kukana chibwenzi mamuna okwatila kuli ngati kukana mabungwe opeleka chithandizo
πππππππππππππππ
Mwana wako wabwela ndi homework, Iweyo wamuthandiza homework ija kenako wakachongetsa ndikukhonza zelo aphunzitsi ndikumuuza kuti mmawa ubwele ndi makolo akoπππ
Muli inu ngati makolo mungapite?
πππππππππ
Osaonesa mtima onyanyalaπ Dzukani phodani muzikaopseza anthu town
ππππππππππππ
Kod azimayi simungatsegule sukulu yophunzisana malilidwe?ππ alamu anu akumatchula maina anthu okufa kuno
ππππππππππππ
Ndimati ndikuuzen kuti Malangizo aja ndawayiwala ndiye mundilangizenso kena
πππππππππππ
Anthu ena akamakuuza kuti ndakutuluka ngati uwafuse kuti kod inuso munali mwa ine?
πππππππππππππ
Mongokumbusana achina ndibwela December mwasala ndi mwezi umodzi okha
ππππππππππππ
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Queen Street
Durban
Alerts
Be the first to know and let us send you an email when MANZY SA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.
